Yesaya 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pa tsiku limenelo, Yehova adzagwiritsa ntchito lupanga lake lakuthwa, lalikulu ndi lolimba,+Kulanga Leviyatani,* njoka yokwawa mothamanga!Adzalanga Leviyatani, njoka yoyenda mokhotakhota,Ndipo adzapha chinjoka chachikulu chokhala mʼnyanja. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:1 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, tsa. 21 Yesaya 1, ptsa. 283-284
27 Pa tsiku limenelo, Yehova adzagwiritsa ntchito lupanga lake lakuthwa, lalikulu ndi lolimba,+Kulanga Leviyatani,* njoka yokwawa mothamanga!Adzalanga Leviyatani, njoka yoyenda mokhotakhota,Ndipo adzapha chinjoka chachikulu chokhala mʼnyanja.