Yesaya 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa tsiku limenelo Yehova adzathyola zipatso kuchokera ku Mtsinje* mpaka kukafika kukhwawa la Iguputo+ ndipo mudzasonkhanitsidwa mmodzimmodzi, inu Aisiraeli.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:12 Yesaya 1, tsa. 285
12 Pa tsiku limenelo Yehova adzathyola zipatso kuchokera ku Mtsinje* mpaka kukafika kukhwawa la Iguputo+ ndipo mudzasonkhanitsidwa mmodzimmodzi, inu Aisiraeli.+