-
Yesaya 28:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Taonani! Yehova ali ndi winawake wamphamvu komanso wanyonga.
Mofanana ndi mvula yamabingu komanso yamatalala, mvula yamphepo yowononga,
Mofanana ndi mvula yamabingu ya madzi amphamvu osefukira,
Iye adzagwetsera pansi chisoti chaulemererocho mwamphamvu.
-