Yesaya 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Yehova ali ndi winawake wamphamvu ndi wanyonga.+ Monga mvula yamabingu ndi yamatalala,+ mvula yamphepo yowononga, ndiponso monga mvula yamabingu ya madzi amphamvu osefukira,+ iye adzagwetsera pansi chisoti chaulemererocho mwamphamvu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:2 Nsanja ya Olonda,1/15/2011, tsa. 36/1/1991, ptsa. 11-12
2 Taonani! Yehova ali ndi winawake wamphamvu ndi wanyonga.+ Monga mvula yamabingu ndi yamatalala,+ mvula yamphepo yowononga, ndiponso monga mvula yamabingu ya madzi amphamvu osefukira,+ iye adzagwetsera pansi chisoti chaulemererocho mwamphamvu.