Yesaya 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova wa makamu adzatembenukira kwa iwe kuti akupulumutse ndi mabingu, zivomezi, phokoso lalikulu, mphepo yamkuntho, ndi lawi la moto wowononga.”+ Nahumu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Adzafafaniza mzinda umenewo+ ndi madzi osefukira ndipo mdima udzathamangitsa adani ake.+
6 Yehova wa makamu adzatembenukira kwa iwe kuti akupulumutse ndi mabingu, zivomezi, phokoso lalikulu, mphepo yamkuntho, ndi lawi la moto wowononga.”+