Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 28:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chilungamo+ ndidzachisandutsa chingwe choyezera+ ndipo ndidzachisandutsanso chipangizo chowongolera.* Mvula yamatalala+ idzakokolola malo othawirapo abodza + ndipo madzi adzasefukira pamalo obisalako.+

  • Ezekieli 13:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndidzatumiza mphepo yamkuntho, mvula yambiri ndi matalala, kusonyeza mkwiyo wanga kuti ndikuwonongeni.+

  • Danieli 9:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Pambuyo pa milungu 62 imeneyi, Mesiya adzaphedwa+ ndipo sadzasiya kalikonse.+

      “Gulu lankhondo la mtsogoleri amene akubwera lidzawononga+ mzindawo ndi malo oyera.+ Malo oyera amenewo adzafafanizidwa ndi madzi osefukira, ndipo padzakhala nkhondo mpaka kumapeto. Mulungu wagamula kuti padzakhale chiwonongeko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena