Salimo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzaweruza anthu padziko lapansi mwachilungamo.+Adzazenga mlandu mitundu ya anthu moyenerera.+ Salimo 35:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Inu Yehova Mulungu wanga, mundiweruze mogwirizana ndi chilungamo chanu,+Musalole kuti adani anga akondwere ndi kusautsika kwanga.+ Yeremiya 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yehova wa makamu amaweruza mwachilungamo.+ Amafufuza impso ndi mtima.+ Inu Mulungu, ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango, pakuti ine ndakufotokozerani mlandu wanga.+
24 Inu Yehova Mulungu wanga, mundiweruze mogwirizana ndi chilungamo chanu,+Musalole kuti adani anga akondwere ndi kusautsika kwanga.+
20 Koma Yehova wa makamu amaweruza mwachilungamo.+ Amafufuza impso ndi mtima.+ Inu Mulungu, ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango, pakuti ine ndakufotokozerani mlandu wanga.+