Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 42:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 ndipo mukapitiriza kunena kuti: “Ife tikupita kukakhala ku Iguputo,+ kumene sitidzaona nkhondo kapena kumva kulira kwa lipenga komanso kumene sitidzasowa chakudya, moti tikupita kukakhala kudziko limenelo,”+

  • Yeremiya 43:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamapeto pake anafika ku Iguputo+ chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo patapita nthawi anakafika ku Tahapanesi.+

  • Ezekieli 17:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma iye anapandukira+ mfumuyo potumiza amithenga ku Iguputo kuti dziko la Iguputo limupatse mahatchi*+ ndi khamu la anthu. Kodi zinthu zidzamuyendera bwino? Kodi munthu amene akuchita zinthu zimenezi ndiponso amene akuphwanya pangano adzapulumuka? Kodi iye adzapulumukadi?’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena