Yesaya 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Yehova ali ndi winawake wamphamvu ndi wanyonga.+ Monga mvula yamabingu ndi yamatalala,+ mvula yamphepo yowononga, ndiponso monga mvula yamabingu ya madzi amphamvu osefukira,+ iye adzagwetsera pansi chisoti chaulemererocho mwamphamvu.
2 Taonani! Yehova ali ndi winawake wamphamvu ndi wanyonga.+ Monga mvula yamabingu ndi yamatalala,+ mvula yamphepo yowononga, ndiponso monga mvula yamabingu ya madzi amphamvu osefukira,+ iye adzagwetsera pansi chisoti chaulemererocho mwamphamvu.