Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 8:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iye adzayang’ana padziko lapansi koma adzangoonapo kuzunzika, mdima,+ kuda, nthawi zovuta ndi zakuda bii, zopanda kuwala.+

  • Yeremiya 13:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Patsani Yehova Mulungu wanu ulemerero+ asanachititse mdima,+ komanso mapazi anu asanapunthwe pamapiri madzulo dzuwa litalowa.+ Mudzayembekeza kuwala+ koma iye adzabweretsa mdima,+ ndipo adzachititsa mdima wandiweyani.+

  • Zefaniya 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsiku limenelo ndi tsiku lamkwiyo, tsiku lansautso ndi zowawa,+ tsiku la mphepo yamkuntho ndi losakaza, tsiku lamdima wochititsa mantha,+ tsiku lamitambo yakuda ndi lamdima wandiweyani.

  • Yuda 6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiponso angelo amene sanasunge malo awo oyambirira koma anasiya malo awo okhala,+ Mulungu anawasunga kosatha m’maunyolo,+ mu mdima wandiweyani kuti adzaweruzidwe pa tsiku lalikulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena