1 Akorinto 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi simukudziwa kuti tidzaweruza angelo?+ Ndiye tingalephere bwanji kuweruza nkhani za m’moyo uno? 2 Petulo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndithu, Mulungu sanalekerere angelo+ amene anachimwa aja osawapatsa chilango, koma mwa kuwaponya mu Tatalasi,*+ anawaika m’maenje a mdima wandiweyani powasungira chiweruzo.+ Chivumbulutso 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo ndinaona mngelo akutsika kuchokera kumwamba ali ndi kiyi wa paphompho+ ndi unyolo waukulu m’dzanja lake.
3 Kodi simukudziwa kuti tidzaweruza angelo?+ Ndiye tingalephere bwanji kuweruza nkhani za m’moyo uno?
4 Ndithu, Mulungu sanalekerere angelo+ amene anachimwa aja osawapatsa chilango, koma mwa kuwaponya mu Tatalasi,*+ anawaika m’maenje a mdima wandiweyani powasungira chiweruzo.+
20 Ndipo ndinaona mngelo akutsika kuchokera kumwamba ali ndi kiyi wa paphompho+ ndi unyolo waukulu m’dzanja lake.