Luka 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ziwandazo zinali kumuchonderera+ kuti asazilamule kuti zipite kuphompho.+ Aefeso 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 chifukwa sitikulimbana+ ndi anthu athupi la magazi ndi nyama ayi, koma ndi maboma,+ maulamuliro,+ olamulira dziko+ a mdimawu, ndi makamu a mizimu yoipa+ m’malo akumwamba. 1 Petulo 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anapita kukalalikira kwa mizimu imene inali m’ndende,+
12 chifukwa sitikulimbana+ ndi anthu athupi la magazi ndi nyama ayi, koma ndi maboma,+ maulamuliro,+ olamulira dziko+ a mdimawu, ndi makamu a mizimu yoipa+ m’malo akumwamba.