4 Ndithu, Mulungu sanalekerere angelo+ amene anachimwa aja osawapatsa chilango, koma mwa kuwaponya mu Tatalasi,*+ anawaika m’maenje a mdima wandiweyani powasungira chiweruzo.+
6 Ndiponso angelo amene sanasunge malo awo oyambirira koma anasiya malo awo okhala,+ Mulungu anawasunga kosatha m’maunyolo,+ mu mdima wandiweyani kuti adzaweruzidwe pa tsiku lalikulu.+