-
Yesaya 28:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kodi iyeyo akufuna kuti aphunzitse ndani,
Ndipo akufuna kuti afotokozere ndani uthengawo kuti aumvetsetse?
Kodi akufuna kufotokozera ana amene asiyitsidwa kumene kuyamwa,
Amene angochotsedwa kumene kubere?
-