Yesaya 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi iyeyo akufuna aphunzitse ndani kudziwa zinthu,+ ndipo akufuna achititse ndani kumvetsetsa uthenga umene wanenedwa?+ Kodi ifeyo akutiyesa ana amene asiya kuyamwa, amene achotsedwa kubere?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:9 Yesaya 1, ptsa. 291-292 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, ptsa. 13-14
9 Kodi iyeyo akufuna aphunzitse ndani kudziwa zinthu,+ ndipo akufuna achititse ndani kumvetsetsa uthenga umene wanenedwa?+ Kodi ifeyo akutiyesa ana amene asiya kuyamwa, amene achotsedwa kubere?+