Yesaya 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Gulu la adani ako* lidzakhala ngati fumbi losalala,+Gulu la olamulira ankhanza lidzakhala ngati mankhusu amene akuuluzika.+ Zimenezi zidzachitika mʼkanthawi kochepa, mosayembekezereka.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:5 Yesaya 1, tsa. 297
5 Gulu la adani ako* lidzakhala ngati fumbi losalala,+Gulu la olamulira ankhanza lidzakhala ngati mankhusu amene akuuluzika.+ Zimenezi zidzachitika mʼkanthawi kochepa, mosayembekezereka.+