-
Yesaya 31:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Chifukwa pa tsiku limenelo, aliyense wa inu adzataya milungu yake yasiliva yomwe ndi yachabechabe komanso milungu yake yagolide yopanda phindu, imene manja anu anapanga nʼkukuchimwitsani.
-