Yesaya 31:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti m’tsiku limenelo, aliyense wa inu adzataya milungu yake yasiliva yachabechabe, ndi milungu yake yagolide yopanda phindu,+ imene manja anu akupangirani n’kukuchimwitsani nayo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:7 Yesaya 1, ptsa. 325-327
7 Pakuti m’tsiku limenelo, aliyense wa inu adzataya milungu yake yasiliva yachabechabe, ndi milungu yake yagolide yopanda phindu,+ imene manja anu akupangirani n’kukuchimwitsani nayo.+