Yesaya 38:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi ndinene kuti chiyani? Iye walankhula ndi ine ndipo wachitapo kanthu. Ndidzayenda modzichepetsa zaka zonse za moyo wangaChifukwa cha kupweteka kwa mtima wanga.*
15 Kodi ndinene kuti chiyani? Iye walankhula ndi ine ndipo wachitapo kanthu. Ndidzayenda modzichepetsa zaka zonse za moyo wangaChifukwa cha kupweteka kwa mtima wanga.*