Yesaya 38:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi ndinene kuti chiyani? Kodi iyeyo andiuza kuti chiyani?+Iyeyonso wachitapo kanthu.+Zaka zanga zonse, ndikungokhalira kuyenda ndili khuma chifukwa cha chisoni cha mtima wanga.+
15 Kodi ndinene kuti chiyani? Kodi iyeyo andiuza kuti chiyani?+Iyeyonso wachitapo kanthu.+Zaka zanga zonse, ndikungokhalira kuyenda ndili khuma chifukwa cha chisoni cha mtima wanga.+