2 Mafumu 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mayiyo atafika kwa munthu wa Mulungu woona paphiripo, nthawi yomweyo anam’gwira mapazi.+ Gehazi ataona zimenezo, anabwera pafupi kuti am’kankhe mayiyo.+ Koma munthu wa Mulungu woonayo+ anamuuza kuti: “Musiye,+ mtima wake ukum’pweteka kwambiri.+ Koma Yehova wandibisira,+ sanandiuze.” Yobu 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho, ine sinditseka pakamwa panga.Ndilankhula chifukwa cha kuvutika mumtima,+Ndilankhula za nkhawa zanga, chifukwa moyo wanga ukupweteka. Yobu 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Winanso adzafa ali wokwiya,Asanadye zinthu zabwino.+ Luka 22:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ndipo anatuluka panja ndi kuyamba kulira mopwetekedwa mtima kwambiri.+
27 Mayiyo atafika kwa munthu wa Mulungu woona paphiripo, nthawi yomweyo anam’gwira mapazi.+ Gehazi ataona zimenezo, anabwera pafupi kuti am’kankhe mayiyo.+ Koma munthu wa Mulungu woonayo+ anamuuza kuti: “Musiye,+ mtima wake ukum’pweteka kwambiri.+ Koma Yehova wandibisira,+ sanandiuze.”
11 Choncho, ine sinditseka pakamwa panga.Ndilankhula chifukwa cha kuvutika mumtima,+Ndilankhula za nkhawa zanga, chifukwa moyo wanga ukupweteka.