1 Samueli 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Hana anali wokhumudwa kwabasi,+ ndipo anayamba kupemphera kwa Yehova+ ndi kulira kwambiri.+ Yobu 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Ineyo ndikunyansidwa ndi moyo wanga.+Ndilankhula mwamphamvu za nkhawa zanga.Ndilankhula chifukwa cha kuwawa kwa moyo wanga. Miyambo 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mtima umadziwa kuwawa kwa moyo wa munthu,+ ndipo mlendo sangalowerere pamene mtimawo ukusangalala.
10 “Ineyo ndikunyansidwa ndi moyo wanga.+Ndilankhula mwamphamvu za nkhawa zanga.Ndilankhula chifukwa cha kuwawa kwa moyo wanga.
10 Mtima umadziwa kuwawa kwa moyo wa munthu,+ ndipo mlendo sangalowerere pamene mtimawo ukusangalala.