Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 11:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ngati umu ndi mmene muchitire ndi ine, ndikomereni mtima chonde, ingondiphani kuti tsokali lindichoke.”+

  • 1 Mafumu 19:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 ndipo iyeyo analowa m’chipululu n’kuyenda ulendo wa tsiku limodzi. Kenako anafika pa kamtengo kenakake,+ ndipo anakhala pansi pake. Ndiyeno anayamba kupempha kuti afe, ponena kuti: “Basi ndatopa nazo. Tsopano chotsani moyo wanga+ Yehova, pakuti sindine woposa makolo anga.”

  • Yobu 7:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Moyo ndaukana,+ sindikufuna kukhala ndi moyo mpaka kalekale.*

      Ndisiyeni chifukwa masiku anga ndi ochepa kwambiri.+

  • Yona 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano inu Yehova, chotsani moyo wanga,+ pakuti kuli bwino kuti ndife kusiyana n’kukhala ndi moyo.”+

  • Aroma 8:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Popeza chilengedwe chinaperekedwa ku mkhalidwe wopanda pake,+ osati mwa kufuna kwake koma kudzera mwa iye amene anachipereka, pa maziko a chiyembekezo+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena