Numeri 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngati umu ndi mmene muchitire ndi ine, ndikomereni mtima chonde, ingondiphani kuti tsokali lindichoke.”+ Yobu 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 N’chifukwa chiyani anthu ena amadikirira imfa, koma siwabwerera,+Ngakhale amakumba pansi poifunafuna, kuposa mmene amakumbira chuma chobisika? Yona 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano inu Yehova, chotsani moyo wanga,+ pakuti kuli bwino kuti ndife kusiyana n’kukhala ndi moyo.”+
15 Ngati umu ndi mmene muchitire ndi ine, ndikomereni mtima chonde, ingondiphani kuti tsokali lindichoke.”+
21 N’chifukwa chiyani anthu ena amadikirira imfa, koma siwabwerera,+Ngakhale amakumba pansi poifunafuna, kuposa mmene amakumbira chuma chobisika?
3 Tsopano inu Yehova, chotsani moyo wanga,+ pakuti kuli bwino kuti ndife kusiyana n’kukhala ndi moyo.”+