Yesaya 57:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Ndikulenga chipatso cha milomo. Mtendere wosatha udzaperekedwa kwa amene ali kutaliNdiponso kwa amene ali pafupi+ ndipo ndidzamʼchiritsa,” akutero Yehova. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 57:19 Yesaya 2, ptsa. 273-274
19 “Ndikulenga chipatso cha milomo. Mtendere wosatha udzaperekedwa kwa amene ali kutaliNdiponso kwa amene ali pafupi+ ndipo ndidzamʼchiritsa,” akutero Yehova.