Yesaya 57:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Ndikulenga chipatso cha milomo.+ Mtendere wosatha udzakhala kwa yemwe ali kutali ndiponso kwa yemwe ali pafupi,+ ndipo ndidzam’chiritsa,”+ akutero Yehova. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 57:19 Yesaya 2, ptsa. 273-274
19 “Ndikulenga chipatso cha milomo.+ Mtendere wosatha udzakhala kwa yemwe ali kutali ndiponso kwa yemwe ali pafupi,+ ndipo ndidzam’chiritsa,”+ akutero Yehova.