Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 48:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!+ Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje,+ ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a m’nyanja.+

  • Luka 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Ulemerero kwa Mulungu kumwambamwamba,+ ndipo pansi pano mtendere+ pakati pa anthu amene iye amakondwera nawo.”+

  • Machitidwe 10:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Mulungu anatumiza mawu+ kwa ana a Isiraeli ndi kulengeza kwa iwo uthenga wabwino wa mtendere+ kudzera mwa Yesu Khristu. Ameneyu ndiye Ambuye wa ena onse.+

  • 2 Akorinto 5:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Chotero ndife+ akazembe+ m’malo mwa Khristu,+ ngati kuti Mulungu akuchonderera anthu kudzera mwa ife.+ Monga okhala m’malo mwa Khristu tikupempha kuti:+ “Gwirizananinso ndi Mulungu.”

  • Aefeso 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chotero iye anabwera n’kulengeza uthenga wabwino wa mtendere+ kwa inuyo, inu akutali, ndipo analengezanso mtendere kwa apafupi,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena