Salimo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+Koma kukoma mtima kwake ndi kwa moyo wonse.+Usiku kumakhala kulira,+ koma m’mawa kumakhala kufuula ndi chisangalalo.+ Yesaya 61:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Wandituma kuti ndikalengeze za chaka cha Yehova chokomera anthu mtima,+ ndi za tsiku lobwezera la Mulungu wathu.+ Wanditumanso kuti ndikatonthoze anthu onse olira,+ Luka 19:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iwo anali kunena kuti: “Wodalitsidwa Iye wobwera monga Mfumu m’dzina la Yehova!+ Mtendere kumwamba, ndi ulemerero kumwambamwambako!”+
5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+Koma kukoma mtima kwake ndi kwa moyo wonse.+Usiku kumakhala kulira,+ koma m’mawa kumakhala kufuula ndi chisangalalo.+
2 Wandituma kuti ndikalengeze za chaka cha Yehova chokomera anthu mtima,+ ndi za tsiku lobwezera la Mulungu wathu.+ Wanditumanso kuti ndikatonthoze anthu onse olira,+
38 Iwo anali kunena kuti: “Wodalitsidwa Iye wobwera monga Mfumu m’dzina la Yehova!+ Mtendere kumwamba, ndi ulemerero kumwambamwambako!”+