Yesaya 62:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo adzatchedwa anthu oyera, anthu amene Yehova anawawombola,+Ndipo iwe udzatchedwa Mzinda Umene Mulungu Anaufunafuna, Mzinda Umene Sanausiyiretu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 62:12 Yesaya 2, tsa. 348
12 Iwo adzatchedwa anthu oyera, anthu amene Yehova anawawombola,+Ndipo iwe udzatchedwa Mzinda Umene Mulungu Anaufunafuna, Mzinda Umene Sanausiyiretu.+