Yesaya 62:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo adzatchedwa anthu oyera,+ owomboledwa ndi Yehova.+ Iweyo udzatchedwa “Mzinda Umene Anaufunafuna,” “Mzinda Umene Sanausiyiretu.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 62:12 Yesaya 2, tsa. 348
12 Iwo adzatchedwa anthu oyera,+ owomboledwa ndi Yehova.+ Iweyo udzatchedwa “Mzinda Umene Anaufunafuna,” “Mzinda Umene Sanausiyiretu.”+