Deuteronomo 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndi kuti adzakukwezani pamwamba pa mitundu ina yonse imene anapanga.+ Zimenezi zidzakudzetserani chitamando, mbiri yabwino ndi kukongola, mukapitiriza kukhala anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu,+ monga mmene anakulonjezerani.” 1 Petulo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma khalani motsanzira Woyera amene anakuitanani. Inunso khalani oyera m’makhalidwe anu onse,+
19 ndi kuti adzakukwezani pamwamba pa mitundu ina yonse imene anapanga.+ Zimenezi zidzakudzetserani chitamando, mbiri yabwino ndi kukongola, mukapitiriza kukhala anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu,+ monga mmene anakulonjezerani.”