Deuteronomo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+ Deuteronomo 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzakukhazikitsani monga anthu ake oyera,+ monga mmene analumbirira kwa inu,+ chifukwa mwapitiriza kusunga malamulo+ a Yehova Mulungu wanu ndipo mwayenda m’njira zake.
6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+
9 Yehova adzakukhazikitsani monga anthu ake oyera,+ monga mmene analumbirira kwa inu,+ chifukwa mwapitiriza kusunga malamulo+ a Yehova Mulungu wanu ndipo mwayenda m’njira zake.