Yesaya 65:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mmbulu ndi mwana wa nkhosa zidzadyera pamodzi,Mkango udzadya udzu ngati ngʼombe yamphongo,+Ndipo chakudya cha njoka chidzakhala fumbi. Zimenezi sizidzapweteka aliyense kapena kuwononga chilichonse mʼphiri langa lonse loyera,”+ akutero Yehova. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:25 Nsanja ya Olonda,9/15/2012, ptsa. 9-104/15/2000, ptsa. 17-18 Yesaya 2, tsa. 388 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 174-175
25 Mmbulu ndi mwana wa nkhosa zidzadyera pamodzi,Mkango udzadya udzu ngati ngʼombe yamphongo,+Ndipo chakudya cha njoka chidzakhala fumbi. Zimenezi sizidzapweteka aliyense kapena kuwononga chilichonse mʼphiri langa lonse loyera,”+ akutero Yehova.
65:25 Nsanja ya Olonda,9/15/2012, ptsa. 9-104/15/2000, ptsa. 17-18 Yesaya 2, tsa. 388 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 174-175