Yeremiya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova anandiuza kuti: “Usanene kuti, ‘Ndine mwana,’ Chifukwa ukuyenera kupita kwa anthu onse kumene ndidzakutume,Ndipo ukanene zonse zimene ndakulamula.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Yeremiya, tsa. 191 Nsanja ya Olonda,4/1/1988, tsa. 10
7 Ndiyeno Yehova anandiuza kuti: “Usanene kuti, ‘Ndine mwana,’ Chifukwa ukuyenera kupita kwa anthu onse kumene ndidzakutume,Ndipo ukanene zonse zimene ndakulamula.+