Yeremiya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Yehova anandiuza kuti: “Usanene kuti, ‘Ndine mwana.’ Koma upite kwa anthu onse amene ndidzakutumako. Ndipo ukanene zonse zimene ndidzakulamula kuti ukanene.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Yeremiya, tsa. 191 Nsanja ya Olonda,4/1/1988, tsa. 10
7 Pamenepo Yehova anandiuza kuti: “Usanene kuti, ‘Ndine mwana.’ Koma upite kwa anthu onse amene ndidzakutumako. Ndipo ukanene zonse zimene ndidzakulamula kuti ukanene.+