Yeremiya 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mayo ine,* mayo ine! Ndikumva kupweteka kwambiri mumtima mwanga. Mtima wanga ukugunda kwambiri. Sindingathe kukhala chete,Chifukwa ndamva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa,Chizindikiro chochenjeza cha nkhondo.*+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:19 Yeremiya, ptsa. 155-156, 182-183 Nsanja ya Olonda,11/1/1994, tsa. 12
19 Mayo ine,* mayo ine! Ndikumva kupweteka kwambiri mumtima mwanga. Mtima wanga ukugunda kwambiri. Sindingathe kukhala chete,Chifukwa ndamva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa,Chizindikiro chochenjeza cha nkhondo.*+