Yeremiya 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 M’mimba mwanga ine, m’mimba mwanga! Ndikumva kupweteka kwambiri mumtima mwanga.+ Mtima wanga ukuvutika.+ Sindingathe kukhala chete pakuti ndamva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, chizindikiro chochenjeza cha nkhondo.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:19 Yeremiya, ptsa. 155-156, 182-183 Nsanja ya Olonda,11/1/1994, tsa. 12
19 M’mimba mwanga ine, m’mimba mwanga! Ndikumva kupweteka kwambiri mumtima mwanga.+ Mtima wanga ukuvutika.+ Sindingathe kukhala chete pakuti ndamva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, chizindikiro chochenjeza cha nkhondo.+