Salimo 42:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 N’chifukwa chiyani ukutaya mtima, moyo wangawe?+Ndipo n’chifukwa chiyani ukusautsika mkati mwanga?+Yembekezera Mulungu,+Ndipo ndidzamutamanda pakuti iye ndiye mpulumutsi wanga wamkulu.+ Yesaya 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 N’chifukwa chake mkati mwanga mukunjenjemera ngati zingwe za zeze chifukwa cha Mowabu,+ ndipo m’mimba mwanga mukubwadamuka chifukwa cha Kiri-hareseti.+
5 N’chifukwa chiyani ukutaya mtima, moyo wangawe?+Ndipo n’chifukwa chiyani ukusautsika mkati mwanga?+Yembekezera Mulungu,+Ndipo ndidzamutamanda pakuti iye ndiye mpulumutsi wanga wamkulu.+
11 N’chifukwa chake mkati mwanga mukunjenjemera ngati zingwe za zeze chifukwa cha Mowabu,+ ndipo m’mimba mwanga mukubwadamuka chifukwa cha Kiri-hareseti.+