Yesaya 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mtima wanga ukulirira Mowabu.+ Anthu ake athawira kutali, ku Zowari+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Aliyense akumakwera mtunda wa Luhiti+ akulira. Panjira yopita ku Horonaimu,+ iwo akufuula kwambiri chifukwa cha tsokalo. Yeremiya 48:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 ‘Choncho mtima wanga udzachitira Mowabu phokoso ngati zitoliro.+ Mtima wanga udzachitira phokoso amuna a ku Kiri-haresi+ ngati zitoliro. Chotero zinthu zochuluka zimene wapanga zidzawonongeka.+
5 Mtima wanga ukulirira Mowabu.+ Anthu ake athawira kutali, ku Zowari+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Aliyense akumakwera mtunda wa Luhiti+ akulira. Panjira yopita ku Horonaimu,+ iwo akufuula kwambiri chifukwa cha tsokalo.
36 ‘Choncho mtima wanga udzachitira Mowabu phokoso ngati zitoliro.+ Mtima wanga udzachitira phokoso amuna a ku Kiri-haresi+ ngati zitoliro. Chotero zinthu zochuluka zimene wapanga zidzawonongeka.+