Miyambo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zamtengo wapatali zidzakhala zopanda phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+ koma chilungamo n’chimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+ Miyambo 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zinthu zamtengo wapatali za munthu wachuma ndizo mzinda wake wolimba,+ ndipo m’maganizo mwake zili ngati mpanda woteteza.+ Yesaya 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 N’chifukwa chake akumanyamula zinthu zotsala ndi katundu amene anasunga, n’kumapita nazo kuchigwa* cha mitengo ya msondodzi. Yeremiya 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu wopeza chuma mopanda chilungamo+ ali ngati nkhwali imene yasonkhanitsa mazira amene sinaikire. Chuma chakecho adzachisiya asanakwanitse ngakhale hafu ya zaka za moyo wake,+ ndipo pamapeto pake adzaonekera kuti ndi wopusa.”+
4 Zinthu zamtengo wapatali zidzakhala zopanda phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+ koma chilungamo n’chimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+
11 Zinthu zamtengo wapatali za munthu wachuma ndizo mzinda wake wolimba,+ ndipo m’maganizo mwake zili ngati mpanda woteteza.+
7 N’chifukwa chake akumanyamula zinthu zotsala ndi katundu amene anasunga, n’kumapita nazo kuchigwa* cha mitengo ya msondodzi.
11 Munthu wopeza chuma mopanda chilungamo+ ali ngati nkhwali imene yasonkhanitsa mazira amene sinaikire. Chuma chakecho adzachisiya asanakwanitse ngakhale hafu ya zaka za moyo wake,+ ndipo pamapeto pake adzaonekera kuti ndi wopusa.”+