Yesaya 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nʼchifukwa chake mkati mwanga mukunjenjemera chifukwa cha Mowabu,+Mukunjenjemera ngati zingwe za zeze,Ndipo mʼmimba mwanga mukunjenjemera chifukwa cha Kiri-hareseti.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:11 Yesaya 1, ptsa. 193-194
11 Nʼchifukwa chake mkati mwanga mukunjenjemera chifukwa cha Mowabu,+Mukunjenjemera ngati zingwe za zeze,Ndipo mʼmimba mwanga mukunjenjemera chifukwa cha Kiri-hareseti.+