Yesaya 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mtima wanga ukulirira Mowabu. Anthu ake athawira kutali, ku Zowari+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Iwo akulira pamene akukwera mtunda wa Luhiti.Panjira yopita ku Horonaimu, iwo akulira kwambiri chifukwa cha tsokalo.+ Yeremiya 48:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 ‘Nʼchifukwa chake mtima wanga udzalirire* Mowabu ngati chitoliro,*+Mtima wanga udzalirira* amuna a ku Kiri-haresi ngati chitoliro.* Chifukwa chuma chimene wapanga chidzawonongeka.
5 Mtima wanga ukulirira Mowabu. Anthu ake athawira kutali, ku Zowari+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Iwo akulira pamene akukwera mtunda wa Luhiti.Panjira yopita ku Horonaimu, iwo akulira kwambiri chifukwa cha tsokalo.+
36 ‘Nʼchifukwa chake mtima wanga udzalirire* Mowabu ngati chitoliro,*+Mtima wanga udzalirira* amuna a ku Kiri-haresi ngati chitoliro.* Chifukwa chuma chimene wapanga chidzawonongeka.