Yesaya 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 N’chifukwa chake mkati mwanga mukunjenjemera ngati zingwe za zeze chifukwa cha Mowabu,+ ndipo m’mimba mwanga mukubwadamuka chifukwa cha Kiri-hareseti.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:11 Yesaya 1, ptsa. 193-194
11 N’chifukwa chake mkati mwanga mukunjenjemera ngati zingwe za zeze chifukwa cha Mowabu,+ ndipo m’mimba mwanga mukubwadamuka chifukwa cha Kiri-hareseti.+