Yeremiya 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yendayendani mʼmisewu ya mu Yerusalemu. Yangʼanani mosamala kwambiri. Fufuzani mʼmabwalo ake kuti muoneNgati mungapeze munthu amene amachita zachilungamo,+Amene amayesetsa kukhala wokhulupirika,Ngati mungamupeze munthu woteroyo, ndidzaukhululukira mzinda umenewu.
5 Yendayendani mʼmisewu ya mu Yerusalemu. Yangʼanani mosamala kwambiri. Fufuzani mʼmabwalo ake kuti muoneNgati mungapeze munthu amene amachita zachilungamo,+Amene amayesetsa kukhala wokhulupirika,Ngati mungamupeze munthu woteroyo, ndidzaukhululukira mzinda umenewu.