Yeremiya 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tamvetserani, mdani akubwera! Kukumveka kugunda kwakukulu kuchokera kudziko lakumpoto,+Kumene kudzasandutsa mizinda ya Yuda kukhala mabwinja, malo obisalamo mimbulu.+
22 Tamvetserani, mdani akubwera! Kukumveka kugunda kwakukulu kuchokera kudziko lakumpoto,+Kumene kudzasandutsa mizinda ya Yuda kukhala mabwinja, malo obisalamo mimbulu.+