-
Yeremiya 23:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Mkwiyo wa Yehova sudzabwerera
Mpaka atachita ndi kukwaniritsa zofuna za mtima wake.
Zinthu zimenezi mudzazimvetsa bwino mʼmasiku otsiriza.
-