Yeremiya 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mkwiyo wa Yehova sudzatha kufikira atachita zofuna za mtima wake+ ndi kuzikwaniritsa.+ M’masiku otsiriza, anthu inu mudzalingalira zimenezi ndipo mudzazimvetsa.+
20 Mkwiyo wa Yehova sudzatha kufikira atachita zofuna za mtima wake+ ndi kuzikwaniritsa.+ M’masiku otsiriza, anthu inu mudzalingalira zimenezi ndipo mudzazimvetsa.+