Levitiko 26:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 pamenepo ndidzatsutsana nanu koopsa,+ ndipo ineyo ndidzakukwapulani maulendo 7 chifukwa cha machimo anu.+ Zekariya 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘“Monga mmene ndinatsimikizira mtima kuchitapo kanthu pamene ndinakugwetserani tsoka chifukwa chakuti makolo anu anandikwiyitsa,+ ndipo sindinakumvereni chisoni,”+ watero Yehova wa makamu,
28 pamenepo ndidzatsutsana nanu koopsa,+ ndipo ineyo ndidzakukwapulani maulendo 7 chifukwa cha machimo anu.+
14 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘“Monga mmene ndinatsimikizira mtima kuchitapo kanthu pamene ndinakugwetserani tsoka chifukwa chakuti makolo anu anandikwiyitsa,+ ndipo sindinakumvereni chisoni,”+ watero Yehova wa makamu,