Zekariya 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘“Monga zinalili kuti ndinatsimikiza mtima kukugwetserani tsoka chifukwa choti makolo anu anandikwiyitsa ndipo sindinakumvereni chisoni,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:14 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, tsa. 20
14 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘“Monga zinalili kuti ndinatsimikiza mtima kukugwetserani tsoka chifukwa choti makolo anu anandikwiyitsa ndipo sindinakumvereni chisoni,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,