Zekariya 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘“Monga mmene ndinatsimikizira mtima kuchitapo kanthu pamene ndinakugwetserani tsoka chifukwa chakuti makolo anu anandikwiyitsa,+ ndipo sindinakumvereni chisoni,”+ watero Yehova wa makamu, Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:14 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, tsa. 20
14 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘“Monga mmene ndinatsimikizira mtima kuchitapo kanthu pamene ndinakugwetserani tsoka chifukwa chakuti makolo anu anandikwiyitsa,+ ndipo sindinakumvereni chisoni,”+ watero Yehova wa makamu,